Danieli 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho Mulungu woona anachititsa kuti mkulu wa nduna zapanyumba ya mfumu akomere mtima Danieli komanso kumusonyeza chifundo.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:9 Ulosi wa Danieli, tsa. 39
9 Choncho Mulungu woona anachititsa kuti mkulu wa nduna zapanyumba ya mfumu akomere mtima Danieli komanso kumusonyeza chifundo.+