Danieli 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mulungu woona anachititsa kuti anyamata* 4 amenewa akhale odziwa zinthu komanso ozindikira zinthu zonse zolembedwa ndipo anawapatsa nzeru. Danieli anamupatsa nzeru zoti azitha kumvetsa bwino masomphenya ndi maloto amtundu uliwonse.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:17 Ulosi wa Danieli, ptsa. 41-42
17 Mulungu woona anachititsa kuti anyamata* 4 amenewa akhale odziwa zinthu komanso ozindikira zinthu zonse zolembedwa ndipo anawapatsa nzeru. Danieli anamupatsa nzeru zoti azitha kumvetsa bwino masomphenya ndi maloto amtundu uliwonse.+