Danieli 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mfumuyo italankhula nawo, inaona kuti pagulu lonselo panalibe aliyense amene ankafanana ndi Danieli, Hananiya, Misayeli ndi Azariya.+ Choncho anyamata amenewa anapitiriza kutumikira mfumu. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:19 Ulosi wa Danieli, ptsa. 42-43
19 Mfumuyo italankhula nawo, inaona kuti pagulu lonselo panalibe aliyense amene ankafanana ndi Danieli, Hananiya, Misayeli ndi Azariya.+ Choncho anyamata amenewa anapitiriza kutumikira mfumu.