Danieli 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pa nkhani iliyonse yofunika nzeru komanso kuzindikira, imene mfumu inkawafunsa, inaona kuti iwo anali anzeru kuwirikiza maulendo 10 kuposa ansembe onse ochita zamatsenga ndi anthu onse olankhula ndi mizimu+ amene anali mu ufumu wake wonse. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:20 Ulosi wa Danieli, ptsa. 43-44 Nsanja ya Olonda,12/1/1988, tsa. 11
20 Pa nkhani iliyonse yofunika nzeru komanso kuzindikira, imene mfumu inkawafunsa, inaona kuti iwo anali anzeru kuwirikiza maulendo 10 kuposa ansembe onse ochita zamatsenga ndi anthu onse olankhula ndi mizimu+ amene anali mu ufumu wake wonse.