Danieli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mʼchaka chachiwiri cha ufumu wake, Nebukadinezara analota maloto angapo, moti anavutika maganizo+ ndipo tulo tinamuthera. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:1 Nsanja ya Olonda,9/1/2007, tsa. 18 Ulosi wa Danieli, ptsa. 46-48
2 Mʼchaka chachiwiri cha ufumu wake, Nebukadinezara analota maloto angapo, moti anavutika maganizo+ ndipo tulo tinamuthera.