Danieli 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Akasidi anayankha mfumu mʼchinenero cha Chiaramu*+ kuti: “Inu mfumu mukhale ndi moyo mpaka kalekale. Tiuzeni ife atumiki anu zimene mwalota ndipo tikumasulirani malotowo.”
4 Akasidi anayankha mfumu mʼchinenero cha Chiaramu*+ kuti: “Inu mfumu mukhale ndi moyo mpaka kalekale. Tiuzeni ife atumiki anu zimene mwalota ndipo tikumasulirani malotowo.”