-
Danieli 2:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Akasidiwo anayankha mfumuyo kuti: “Palibe munthu padziko lapansi amene angathe kuchita zimene inu mfumu mukufuna. Palibe mfumu yaikulu kapena bwanamkubwa amene anauzapo wansembe wochita zamatsenga, munthu wolankhula ndi mizimu kapena Mkasidi kuti achite zimenezi.
-