-
Danieli 2:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Zimene inu mfumu mukufuna kuti tichite ndi zovuta, ndipo palibe munthu amene angakuuzeni maloto anu kupatulapo milungu, imene sikhala pakati pa anthu.”
-