-
Danieli 2:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Iye anawapempha kuti apemphere kwa Mulungu wakumwamba kuti awachitire chifundo nʼkuwaululira chinsinsi chimenechi, kuti Danieli ndi anzakewo asaphedwe limodzi ndi amuna ena onse anzeru a mʼBabulo.
-