Danieli 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma kumwamba kuli Mulungu amene ndi Woulula zinsinsi,+ ndipo wakudziwitsani inu Mfumu Nebukadinezara zimene zidzachitike mʼmasiku otsiriza. Maloto anu komanso masomphenya amene munaona muli pabedi lanu ndi awa: Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:28 Ulosi wa Danieli, ptsa. 48-49 Nsanja ya Olonda,11/15/1986, tsa. 6
28 Koma kumwamba kuli Mulungu amene ndi Woulula zinsinsi,+ ndipo wakudziwitsani inu Mfumu Nebukadinezara zimene zidzachitike mʼmasiku otsiriza. Maloto anu komanso masomphenya amene munaona muli pabedi lanu ndi awa: