Danieli 2:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Sikuti chinsinsi chimenechi chaululidwa kwa ine chifukwa chakuti ndine wanzeru kuposa munthu wina aliyense, koma chaululidwa nʼcholinga chakuti ndikumasulireni malotowo inu mfumu ndiponso kuti mudziwe maganizo amumtima mwanu.+
30 Sikuti chinsinsi chimenechi chaululidwa kwa ine chifukwa chakuti ndine wanzeru kuposa munthu wina aliyense, koma chaululidwa nʼcholinga chakuti ndikumasulireni malotowo inu mfumu ndiponso kuti mudziwe maganizo amumtima mwanu.+