Danieli 2:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Munapitiriza kuyangʼana mpaka mwala unadulidwa kuphiri koma osati ndi manja a munthu. Mwalawo unamenya chifanizirocho kumapazi ake achitsulo chosakanikirana ndi dongo nʼkuwaphwanya.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:34 Ulosi wa Danieli, ptsa. 60-62 Galamukani!,1/8/1991, tsa. 29 Nsanja ya Olonda,11/15/1986, tsa. 7
34 Munapitiriza kuyangʼana mpaka mwala unadulidwa kuphiri koma osati ndi manja a munthu. Mwalawo unamenya chifanizirocho kumapazi ake achitsulo chosakanikirana ndi dongo nʼkuwaphwanya.+