Danieli 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mfumu Nebukadinezara inapanga fano lagolide limene linali lalitali mikono 60* ndipo mulifupi mwake linali mikono 6.* Fanoli analiimika mʼchigwa cha Dura, mʼchigawo cha Babulo. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:1 Ulosi wa Danieli, tsa. 72
3 Mfumu Nebukadinezara inapanga fano lagolide limene linali lalitali mikono 60* ndipo mulifupi mwake linali mikono 6.* Fanoli analiimika mʼchigwa cha Dura, mʼchigawo cha Babulo.