-
Danieli 3:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 kuti mukangomva kulira kwa lipenga, chitoliro, zeze wamngʼono, zeze wamakona atatu, choimbira chazingwe, chitoliro chathumba ndi zipangizo zina zonse zoimbira, mugwade nʼkuwerama mpaka nkhope zanu pansi ndipo mulambire fano lagolide limene Mfumu Nebukadinezara yaimika.
-