-
Danieli 3:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Inuyo mfumu munalamula kuti munthu aliyense akamva kulira kwa lipenga, chitoliro, zeze wamngʼono, zeze wamakona atatu, choimbira chazingwe, chitoliro chathumba ndi zipangizo zina zonse zoimbira, agwade nʼkulambira fano lagolide.
-