Danieli 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munalamulanso kuti aliyense amene sagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi nʼkulambira fanolo aponyedwe mungʼanjo yoyaka moto.+
11 Munalamulanso kuti aliyense amene sagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi nʼkulambira fanolo aponyedwe mungʼanjo yoyaka moto.+