-
Danieli 3:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndiyeno Nebukadinezara anapsa mtima kwambiri ndipo analamula kuti abweretse Shadireki, Misheki ndi Abedinego. Choncho anabweretsadi amuna amenewa pamaso pa mfumu.
-