-
Danieli 3:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ndiye Shadireki, Misheki ndi Abedinego anayankha mfumuyo kuti: “Inu Mfumu Nebukadinezara, palibenso china chimene ife tinganene kwa inu pa nkhani imeneyi.
-