Danieli 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamenepo Nebukadinezara anapsa mtima kwambiri ndi Shadireki, Misheki ndi Abedinego ndipo nkhope yake inasintha.* Iye analamula kuti ngʼanjoyo aisonkhezere kuwirikiza ka 7 kuposa mmene ankachitira nthawi zonse. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:19 Nsanja ya Olonda,12/1/1988, tsa. 19
19 Pamenepo Nebukadinezara anapsa mtima kwambiri ndi Shadireki, Misheki ndi Abedinego ndipo nkhope yake inasintha.* Iye analamula kuti ngʼanjoyo aisonkhezere kuwirikiza ka 7 kuposa mmene ankachitira nthawi zonse.