-
Danieli 3:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Ndiyeno mfumu inati: “Taonani! Inetu ndikuona amuna 4 akuyendayenda pakati pa moto ali osamangidwa komanso sakupsa, ndipo munthu wa 4 akuoneka ngati mwana wa milungu.”
-