27 Masatarapi, akuluakulu a boma, abwanamkubwa ndi nduna zapamwamba za mfumu amene anasonkhana kumeneko,+ anaona kuti amuna amenewa+ motowo sunawawotche ngakhale pangʼono. Tsitsi la kumutu kwawo ndi limodzi lomwe silinawauke. Zovala zawo sizinasinthe ndipo sankamveka ngakhale fungo la moto.