-
Danieli 3:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Choncho ine ndikuika lamulo lakuti, anthu a mtundu uliwonse kapena olankhula zinenero zosiyanasiyana amene anganene chilichonse chotsutsana ndi Mulungu wa Shadireki, Misheki ndi Abedinego ayenera kudulidwa nthulinthuli ndipo nyumba zawo zisandutsidwe zimbudzi za anthu onse,* chifukwa palibe mulungu wina amene amatha kupulumutsa anthu ake mofanana ndi ameneyu.”+
-