-
Danieli 4:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ine Nebukadinezara ndinkakhala mwabata mʼnyumba mwanga ndipo zinthu zinkandiyendera bwino mʼnyumba yanga yachifumu.
-