Danieli 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno ndinalota maloto amene anandichititsa mantha. Nditagona pabedi langa ndinaona zithunzithunzi ndi masomphenya zimene zinandichititsa mantha.+
5 Ndiyeno ndinalota maloto amene anandichititsa mantha. Nditagona pabedi langa ndinaona zithunzithunzi ndi masomphenya zimene zinandichititsa mantha.+