Danieli 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawi imeneyo ansembe ochita zamatsenga, anthu olankhula ndi mizimu, Akasidi* ndi okhulupirira nyenyezi+ anabwera kwa ine. Nditawafotokozera malotowo, sanathe kundiuza kumasulira kwake.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2139
7 Pa nthawi imeneyo ansembe ochita zamatsenga, anthu olankhula ndi mizimu, Akasidi* ndi okhulupirira nyenyezi+ anabwera kwa ine. Nditawafotokozera malotowo, sanathe kundiuza kumasulira kwake.+