-
Danieli 4:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Masamba ake anali okongola ndipo unali ndi zipatso zambiri, moti anthu ndi nyama ankapezamo chakudya chokwanira. Nyama zakutchire zinkakhala mumthunzi wake ndipo mbalame zamumlengalenga zinkakhala munthambi zake. Zamoyo zonse zinkapeza chakudya mumtengowo.
-