Danieli 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mlondayo analankhula mofuula kuti: “Gwetsani mtengowo+ ndipo mudule nthambi zake. Yoyolani masamba ake ndipo mumwaze zipatso zake. Nyama zithawe pansi pake ndipo mbalame zichoke panthambi zake. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:14 Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 138-140 Mtendere Weniweni, ptsa. 71-72
14 Mlondayo analankhula mofuula kuti: “Gwetsani mtengowo+ ndipo mudule nthambi zake. Yoyolani masamba ake ndipo mumwaze zipatso zake. Nyama zithawe pansi pake ndipo mbalame zichoke panthambi zake.