Danieli 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma musiye chitsa ndi mizu yake munthaka ndipo muchikulunge ndi mkombero wachitsulo komanso wakopa.* Chikhale pakati pa udzu wakutchire ndipo chizinyowa ndi mame akumwamba. Chikhalenso pakati pa nyama zakutchire ndi udzu wapadziko lapansi.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:15 Ulosi wa Danieli, ptsa. 85-86, 90-92 Mtendere Weniweni, ptsa. 71-72
15 Koma musiye chitsa ndi mizu yake munthaka ndipo muchikulunge ndi mkombero wachitsulo komanso wakopa.* Chikhale pakati pa udzu wakutchire ndipo chizinyowa ndi mame akumwamba. Chikhalenso pakati pa nyama zakutchire ndi udzu wapadziko lapansi.+