Danieli 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Inu munaona mtengo umene unakula kwambiri ndipo unakhala wamphamvu. Nsonga ya mtengowo inakafika mpaka kumwamba ndipo unkaoneka padziko lonse lapansi.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:20 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 32 Nsanja ya Olonda,9/1/2007, ptsa. 18-19
20 Inu munaona mtengo umene unakula kwambiri ndipo unakhala wamphamvu. Nsonga ya mtengowo inakafika mpaka kumwamba ndipo unkaoneka padziko lonse lapansi.+