Danieli 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Masamba ake anali okongola ndipo unali ndi zipatso zambiri. Mumtengomo munali zakudya zokwanira anthu ndi nyama zonse. Nyama zakutchire zinkakhala pansi pake ndipo mbalame zamumlengalenga zinkakhala munthambi zake.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:21 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 32
21 Masamba ake anali okongola ndipo unali ndi zipatso zambiri. Mumtengomo munali zakudya zokwanira anthu ndi nyama zonse. Nyama zakutchire zinkakhala pansi pake ndipo mbalame zamumlengalenga zinkakhala munthambi zake.+