Danieli 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma chifukwa ananena kuti asiye chitsa cha mtengowo ndi mizu yake,+ inu mudzayambiranso kulamulira mu ufumu wanu mutadziwa kuti Mulungu ndi amene akulamulira kumwamba. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:26 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 32 Ulosi wa Danieli, tsa. 88
26 Koma chifukwa ananena kuti asiye chitsa cha mtengowo ndi mizu yake,+ inu mudzayambiranso kulamulira mu ufumu wanu mutadziwa kuti Mulungu ndi amene akulamulira kumwamba.