27 Choncho inu mfumu, mverani malangizo anga. Musiye kuchita machimo ndipo muzichita zinthu zabwino. Musiyenso kuchita zinthu zoipa ndipo muzichitira chifundo anthu osauka. Mukatero, mwina zinthu zidzapitiriza kukuyenderani bwino kwa nthawi yaitali.’”+