Danieli 4:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Tsopano ine Nebukadinezara ndikutamanda, kukweza ndi kulemekeza Mfumu yakumwamba,+ chifukwa ntchito zake zonse ndi zogwirizana ndi choonadi, njira zake ndi zolungama+ ndiponso amatha kutsitsa anthu onyada.”+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:37 Ulosi wa Danieli, tsa. 93 Nsanja ya Olonda,12/1/1988, tsa. 13
37 Tsopano ine Nebukadinezara ndikutamanda, kukweza ndi kulemekeza Mfumu yakumwamba,+ chifukwa ntchito zake zonse ndi zogwirizana ndi choonadi, njira zake ndi zolungama+ ndiponso amatha kutsitsa anthu onyada.”+