Danieli 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Belisazara ataledzera ndi vinyoyo analamula kuti abweretse ziwiya zagolide ndi zasiliva zimene Nebukadinezara bambo ake anatenga mʼkachisi ku Yerusalemu.+ Anachita zimenezi kuti mfumuyo, nduna zake, adzakazi* ake ndi akazi ake ena amweremo. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:2 Ulosi wa Danieli, tsa. 101
2 Belisazara ataledzera ndi vinyoyo analamula kuti abweretse ziwiya zagolide ndi zasiliva zimene Nebukadinezara bambo ake anatenga mʼkachisi ku Yerusalemu.+ Anachita zimenezi kuti mfumuyo, nduna zake, adzakazi* ake ndi akazi ake ena amweremo.