Danieli 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo anamwa vinyo nʼkuyamba kutamanda milungu yagolide, yasiliva, yakopa,* yachitsulo, yamitengo ndi yamiyala. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:4 Ulosi wa Danieli, tsa. 101 Nsanja ya Olonda,2/1/1988, ptsa. 12-13
4 Iwo anamwa vinyo nʼkuyamba kutamanda milungu yagolide, yasiliva, yakopa,* yachitsulo, yamitengo ndi yamiyala.