-
Danieli 5:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Nthawi yomweyo, dzanja la munthu linaonekera ndipo linayamba kulemba pakhoma lapulasitala la nyumba ya mfumu, pafupi ndi choikapo nyale ndipo mfumuyo inaona dzanja limene linkalembalo.
-