Danieli 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno nkhope ya mfumuyo inasintha ndipo iye anachita mantha kwambiri. Miyendo komanso mawondo+ ake anayamba kunjenjemera. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:6 Ulosi wa Danieli, ptsa. 102-104
6 Ndiyeno nkhope ya mfumuyo inasintha ndipo iye anachita mantha kwambiri. Miyendo komanso mawondo+ ake anayamba kunjenjemera.