-
Danieli 5:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ndiye mfumuyo inaitana mofuula olankhula ndi mizimu, Akasidi* ndi okhulupirira nyenyezi.+ Mfumuyo inauza amuna anzeru a mʼBabulo amenewa kuti: “Aliyense amene angawerenge mawuwa nʼkundiuza kumasulira kwake, ndimuveka zovala zapepo ndi mkanda wagolide mʼkhosi+ ndipo akhala wolamulira wachitatu mu ufumuwu.”+
-