Danieli 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amuna onse anzeru anabwera kwa mfumu koma sanathe kuwerenga mawu amene analembedwawo kapena kuuza mfumu kumasulira kwake.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:8 Ulosi wa Danieli, ptsa. 104-105
8 Amuna onse anzeru anabwera kwa mfumu koma sanathe kuwerenga mawu amene analembedwawo kapena kuuza mfumu kumasulira kwake.+