-
Danieli 5:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Mfumukazi itamva mawu a mfumu ndi a nduna zake, inalowa mʼchipinda chimene ankachitira phwandolo. Mfumukaziyo inati: “Inu mfumu, mukhale ndi moyo mpaka kalekale. Musachite mantha komanso nkhope yanu isasinthe.
-