Danieli 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndamva kuti mwa iwe muli mzimu wa milungu+ ndiponso kuti uli ndi luso lodabwitsa, ndiwe wozindikira komanso kuti uli ndi nzeru zodabwitsa.+
14 Ndamva kuti mwa iwe muli mzimu wa milungu+ ndiponso kuti uli ndi luso lodabwitsa, ndiwe wozindikira komanso kuti uli ndi nzeru zodabwitsa.+