16 Koma ndamva kuti iweyo umatha kumasulira zinthu+ komanso kuthana ndi zinthu zovuta. Ndiye ngati ungathe kuwerenga mawuwa nʼkundiuza kumasulira kwake, ndikuveka zovala zapepo ndi mkanda wagolide mʼkhosi mwako ndipo ukhala wolamulira wachitatu mu ufumuwu.”+