-
Danieli 5:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Ndiyeno Danieli anayankha mfumuyo kuti: “Mphatso zanuzo mukhoza kusunga ndipo mphoto zanuzo mupatse ena. Komabe, inu mfumu, ndikuwerengerani mawu amene alembedwawa ndipo ndikuuzani kumasulira kwake.
-