Danieli 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Inu mfumu, Mulungu Wamʼmwambamwamba anapatsa bambo anu Nebukadinezara ufumu, ukulu, ulemu ndi ulemerero.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:18 Ulosi wa Danieli, ptsa. 15-17
18 Inu mfumu, Mulungu Wamʼmwambamwamba anapatsa bambo anu Nebukadinezara ufumu, ukulu, ulemu ndi ulemerero.+