Danieli 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma pamene mtima wake unayamba kudzikuza ndiponso pamene anaumitsa mtima wake nʼkuchita zinthu modzikweza,+ anatsitsidwa pampando wake wachifumu ndipo ulemerero wake unachotsedwa.
20 Koma pamene mtima wake unayamba kudzikuza ndiponso pamene anaumitsa mtima wake nʼkuchita zinthu modzikweza,+ anatsitsidwa pampando wake wachifumu ndipo ulemerero wake unachotsedwa.