-
Danieli 5:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Koma inuyo a Belisazara, amene ndinu mwana wake, simunadzichepetse mumtima mwanu ngakhale kuti mukudziwa zonsezi.
-