Danieli 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno Belisazara analamula kuti Danieli avekedwe zovala zapepo ndi mkanda wagolide mʼkhosi mwake. Ndipo analengeza kuti Danieli akhala wolamulira wachitatu mu ufumuwo.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:29 Ulosi wa Danieli, ptsa. 109-110 Nsanja ya Olonda,10/1/1988, tsa. 30
29 Ndiyeno Belisazara analamula kuti Danieli avekedwe zovala zapepo ndi mkanda wagolide mʼkhosi mwake. Ndipo analengeza kuti Danieli akhala wolamulira wachitatu mu ufumuwo.+