Danieli 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anaikanso nduna zapamwamba zitatu kuti ziziyangʼanira masatarapiwo ndipo Danieli anali mmodzi wa ndunazo.+ Masatarapiwo+ ankayenera kuuza nduna zimenezi chilichonse chimene chikuchitika nʼcholinga chakuti zinthu za mfumu zisawonongeke. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:2 Ulosi wa Danieli, ptsa. 115-116
2 Anaikanso nduna zapamwamba zitatu kuti ziziyangʼanira masatarapiwo ndipo Danieli anali mmodzi wa ndunazo.+ Masatarapiwo+ ankayenera kuuza nduna zimenezi chilichonse chimene chikuchitika nʼcholinga chakuti zinthu za mfumu zisawonongeke.