Danieli 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Danieli anaonetsa kuti anali wodziwa kugwira ntchito bwino kuposa nduna zina zapamwamba ndi masatarapi, chifukwa anali ndi luso lodabwitsa+ ndipo mfumu inaganiza zomukweza kuti akhale ndi udindo waukulu mu ufumu wonsewo. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:3 Ulosi wa Danieli, tsa. 116
3 Ndiyeno Danieli anaonetsa kuti anali wodziwa kugwira ntchito bwino kuposa nduna zina zapamwamba ndi masatarapi, chifukwa anali ndi luso lodabwitsa+ ndipo mfumu inaganiza zomukweza kuti akhale ndi udindo waukulu mu ufumu wonsewo.