-
Danieli 6:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Nduna zonse zapamwamba za mu ufumu uno, akuluakulu a boma, masatarapi, alangizi a mfumu ndi abwanamkubwa agwirizana kuti inu mfumu mukhazikitse lamulo loletsa munthu aliyense kupemphera kwa mulungu kapena kwa munthu wina aliyense kwa masiku 30, kupatulapo kwa inu nokha mfumu. Aliyense amene samvera lamulo limeneli aponyedwe mʼdzenje la mikango.+
-